Yobu 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye akalanda chinthu, ndani angalimbane naye? Ndani angamufunse kuti, ‘Mukuchita chiyani?’+