Yobu 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa iye wandivulaza ndi mavuto angati mphepo yamkuntho,Ndipo wachulukitsa mabala anga popanda chifukwa.+
17 Chifukwa iye wandivulaza ndi mavuto angati mphepo yamkuntho,Ndipo wachulukitsa mabala anga popanda chifukwa.+