Yobu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zonsezi mfundo yake ndi imodzi. Nʼchifukwa chake ndikunena kuti,‘Iye amawononga onse, osalakwa* komanso oipa.’
22 Zonsezi mfundo yake ndi imodzi. Nʼchifukwa chake ndikunena kuti,‘Iye amawononga onse, osalakwa* komanso oipa.’