Yobu 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Panopa masiku anga akufulumira kwambiri kuposa munthu wothamanga.+Iwo akuthawa asanaone zabwino.