Yobu 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Moyo wanga ndikunyansidwa nawo.+ Ndinena madandaulo anga mwamphamvu. Ndilankhula mopwetekedwa mtima.* Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:1 Nsanja ya Olonda,3/15/2006, tsa. 15
10 “Moyo wanga ndikunyansidwa nawo.+ Ndinena madandaulo anga mwamphamvu. Ndilankhula mopwetekedwa mtima.*