Yobu 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Manja anu ndi amene anandiumba ndiponso kundipanga,+Koma tsopano mukufuna kundiwonongeratu.