Yobu 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiye nʼchifukwa chiyani munanditulutsa mʼmimba mwa mayi anga?+ Zikanakhala bwino ndikanafa diso lililonse lisanandione.
18 Ndiye nʼchifukwa chiyani munanditulutsa mʼmimba mwa mayi anga?+ Zikanakhala bwino ndikanafa diso lililonse lisanandione.