Yobu 11:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi zolankhula zako zopanda pake zingachititse kuti anthu akhale chete? Kodi sipapezeka wokudzudzula chifukwa cha mawu ako onyoza?+
3 Kodi zolankhula zako zopanda pake zingachititse kuti anthu akhale chete? Kodi sipapezeka wokudzudzula chifukwa cha mawu ako onyoza?+