Yobu 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu akuba amakhala mwamtendere mʼmatenti awo,+Amene amakwiyitsa Mulungu amakhala otetezeka,+Anthu amene mulungu wawo ali mʼmanja mwawo.
6 Anthu akuba amakhala mwamtendere mʼmatenti awo,+Amene amakwiyitsa Mulungu amakhala otetezeka,+Anthu amene mulungu wawo ali mʼmanja mwawo.