Yobu 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye akagwetsa chinthu, sichingamangidwenso,+Zimene iye watseka, palibe munthu amene angatsegule.