Yobu 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotsani dzanja lanu lolemera nʼkuliika kutali kwambiri ndi ine,Ndipo musapitirize kundiopseza.+