-
Yobu 14:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Madzi amaperepesa miyala
Ndipo mitsinje yake imakokolola dothi lapadziko lapansi.
Inunso mwawononga chiyembekezo cha munthu.
-