Yobu 15:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zimene anthu anzeru amanena,Zinthu zimene anamva kuchokera kwa makolo awo ndipo sanazibise.+