Yobu 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma sindikanatero, mʼmalomwake ndikanakulimbikitsani ndi mawu amʼkamwa mwanga,Ndipo mawu otonthoza apakamwa panga akanakulimbikitsani.+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:5 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,4/2016, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,3/15/1990, tsa. 27
5 Koma sindikanatero, mʼmalomwake ndikanakulimbikitsani ndi mawu amʼkamwa mwanga,Ndipo mawu otonthoza apakamwa panga akanakulimbikitsani.+