Yobu 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndikalankhula, ululu wanga sukuchepa,+Ndipo ndikasiya kulankhula, ululu wanga sukutha.