Yobu 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mkwiyo wa Mulungu wandikhadzula ndipo akundisungira chidani.+ Iye akundikukutira mano. Mdani wanga akundiyangʼana mokwiya nʼcholinga choti andivulaze.+
9 Mkwiyo wa Mulungu wandikhadzula ndipo akundisungira chidani.+ Iye akundikukutira mano. Mdani wanga akundiyangʼana mokwiya nʼcholinga choti andivulaze.+