Yobu 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu ake oponya mivi ndi uta andizungulira.+Iye waboola impso zanga+ ndipo sakumva chisoni,Wakhuthulira ndulu yanga pansi.
13 Anthu ake oponya mivi ndi uta andizungulira.+Iye waboola impso zanga+ ndipo sakumva chisoni,Wakhuthulira ndulu yanga pansi.