Yobu 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye wachititsa kuti anthu azindinyoza,+Mwakuti ndakhala munthu amene anthu akumulavulira kumaso.+