Yobu 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndidzaitana dzenje*+ kuti, ‘Ndinu bambo anga!’ Kwa mphutsi ndidzati, ‘Mayi anga ndi mlongo wanga!’
14 Ndidzaitana dzenje*+ kuti, ‘Ndinu bambo anga!’ Kwa mphutsi ndidzati, ‘Mayi anga ndi mlongo wanga!’