-
Yobu 20:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Pamene akudzazitsa mimba yake,
Mulungu adzamutumizira mkwiyo wake woyaka moto,
Adzauvumbitsa pa iye mpaka udzafika mʼmatumbo mwake.
-