Yobu 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ndikudziwa kuti alibe mphamvu zochititsa kuti zinthu ziwayendere bwino pa moyo wawo.+ Zimene anthu oipa amaganiza nʼzosiyana* ndi zimene ndimaganiza.+
16 Koma ndikudziwa kuti alibe mphamvu zochititsa kuti zinthu ziwayendere bwino pa moyo wawo.+ Zimene anthu oipa amaganiza nʼzosiyana* ndi zimene ndimaganiza.+