Yobu 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Akatsimikiza kuti achite zinthu, ndi ndani angamuletse?+ Akafuna kuchita chinthu, amachitadi.+