Yobu 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komatu zimenezi ndi kambali kakangʼono chabe ka zochita zake,+Ndipo tangomva kunongʼona kwapansipansi kwa mphamvu zake. Ndiye ndi ndani amene angamvetse mabingu ake amphamvu?”+
14 Komatu zimenezi ndi kambali kakangʼono chabe ka zochita zake,+Ndipo tangomva kunongʼona kwapansipansi kwa mphamvu zake. Ndiye ndi ndani amene angamvetse mabingu ake amphamvu?”+