Yobu 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndinali bambo kwa osauka,+Ndipo ndinkafufuza mlandu wa anthu amene sindinkawadziwa.+