Yobu 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinkawapatsa malangizo ngati mtsogoleri wawo,Ndinkakhala ngati mfumu imene ili pakati pa asilikali ake,+Ndinali ngati wotonthoza anthu amene akulira.”+
25 Ndinkawapatsa malangizo ngati mtsogoleri wawo,Ndinkakhala ngati mfumu imene ili pakati pa asilikali ake,+Ndinali ngati wotonthoza anthu amene akulira.”+