Yobu 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Tsopano anthu amene ndi aangʼono kwa ine,Akundiseka.+Anthu amene abambo awo sindikanalolaKuwaika pamodzi ndi agalu olondera nkhosa zanga.
30 “Tsopano anthu amene ndi aangʼono kwa ine,Akundiseka.+Anthu amene abambo awo sindikanalolaKuwaika pamodzi ndi agalu olondera nkhosa zanga.