Yobu 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma pano amandinyoza ngakhale akamaimba nyimbo zawo,+Ndakhala chinthu choseketsa* kwa iwo.+