Yobu 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho Elihu mwana wa Barakeli mbadwa ya Buza, anayamba kulankhula kuti: “Ine ndine wamngʼono*Ndipo amuna inu ndinu achikulire.+ Nʼchifukwa chake mwaulemu ndinakhala chete,+Ndipo sindinayese nʼkomwe kukuuzani zimene ndikudziwa.
6 Choncho Elihu mwana wa Barakeli mbadwa ya Buza, anayamba kulankhula kuti: “Ine ndine wamngʼono*Ndipo amuna inu ndinu achikulire.+ Nʼchifukwa chake mwaulemu ndinakhala chete,+Ndipo sindinayese nʼkomwe kukuuzani zimene ndikudziwa.