Yobu 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma mzimu umene uli mwa anthu,Mpweya wa Wamphamvuyonse, ndi umene umawathandiza kuti azimvetsa zinthu.+
8 Koma mzimu umene uli mwa anthu,Mpweya wa Wamphamvuyonse, ndi umene umawathandiza kuti azimvetsa zinthu.+