Yobu 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inetu ndimadikira kuti inu mumalize kulankhula.Ndakhala ndikumvetsera mfundo zanu+Pamene mumafufuza zoti munene.+
11 Inetu ndimadikira kuti inu mumalize kulankhula.Ndakhala ndikumvetsera mfundo zanu+Pamene mumafufuza zoti munene.+