Yobu 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Moti amaipidwa* ndi chakudya,Ndipo iye amakana* ngakhale chakudya chabwino.+