Yobu 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chifukwa wanena kuti, ‘Munthu sapindula chilichonseAkamayesetsa kuchita zosangalatsa Mulungu.’+