Yobu 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho ndimvetsereni, inu amuna omvetsa zinthu:* Nʼzosatheka kuti Mulungu woona achite zoipa,+Kapena kuti Wamphamvuyonse achite zinthu zolakwika.+
10 Choncho ndimvetsereni, inu amuna omvetsa zinthu:* Nʼzosatheka kuti Mulungu woona achite zoipa,+Kapena kuti Wamphamvuyonse achite zinthu zolakwika.+