Yobu 34:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndithudi, Mulungu sachita zoipa,+Ndipo Wamphamvuyonse sakhotetsa chilungamo.+