Yobu 34:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi mungauze mfumu kuti, ‘Ndinu wopanda pake,’ Kapena anthu olemekezeka kuti, ‘Ndinu oipaʼ?+