Yobu 34:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Maso a Mulungu amayangʼanitsitsa njira za munthu,+Ndipo amaona chilichonse chimene akuchita.