Yobu 34:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chifukwa iye akudziwa zimene iwo akuchita.+Iye amawagonjetsa usiku ndipo iwo amaphwanyika.+