-
Yobu 34:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Ngati Mulungu atakhala chete, ndi ndani angamudzudzule?
Ngati atabisa nkhope yake, ndi ndani angamuone?
Kaya abisire nkhope yake mtundu wa anthu kapena munthu mmodzi, zotsatira zake nʼchimodzimodzi.
-