-
Yobu 34:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Kodi ukufuna kuti akupatse mphoto mogwirizana ndi mmene iweyo ukuonera, pamene ukukana chiweruzo chake?
Iweyo usankhe wekha, osati ine.
Choncho ndiuze zimene ukuzidziwa bwino.
-