Yobu 35:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ngati anthu akuponderezedwa kwambiri, amalira kuti athandizidwe.Amalira kuti apulumutsidwe mʼmanja mwa anthu amphamvu amene akuwapondereza.+
9 Ngati anthu akuponderezedwa kwambiri, amalira kuti athandizidwe.Amalira kuti apulumutsidwe mʼmanja mwa anthu amphamvu amene akuwapondereza.+