Yobu 36:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu oipa mtima* adzasunga chakukhosi. Iwo sapempha thandizo ngakhale Mulungu atawamanga.