Yobu 37:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa amauza matalala kuti, ‘Gwerani padziko lapansi,’+ Ndipo mvula amaiuza kuti, ‘Igwa mwamphamvu kwambiri.’+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:6 Nsanja ya Olonda,4/15/2001, tsa. 4
6 Chifukwa amauza matalala kuti, ‘Gwerani padziko lapansi,’+ Ndipo mvula amaiuza kuti, ‘Igwa mwamphamvu kwambiri.’+