Yobu 37:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amagwiritsa ntchito mitamboyo kuti apereke chilango,*+ kuti anyowetse dziko,Komanso kuti asonyeze chikondi chokhulupirika.+
13 Amagwiritsa ntchito mitamboyo kuti apereke chilango,*+ kuti anyowetse dziko,Komanso kuti asonyeze chikondi chokhulupirika.+