Yobu 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kodi mukudziwa chimene chimachititsa kuti mitambo izikhala mʼmalere?+ Zimenezi ndi ntchito zodabwitsa za Mulungu amene amadziwa chilichonse.+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:16 Nsanja ya Olonda,6/15/1993, tsa. 9
16 Kodi mukudziwa chimene chimachititsa kuti mitambo izikhala mʼmalere?+ Zimenezi ndi ntchito zodabwitsa za Mulungu amene amadziwa chilichonse.+