Yobu 37:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iwo sangathe nʼkomwe kuona kuwala,*Ngakhale kuti kuthambo nʼkowala,Mpaka mphepo itadutsa nʼkuchotsa mitambo.
21 Iwo sangathe nʼkomwe kuona kuwala,*Ngakhale kuti kuthambo nʼkowala,Mpaka mphepo itadutsa nʼkuchotsa mitambo.