Yobu 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Wamphamvuyonse sitingathe kumumvetsa.+Iye ali ndi mphamvu zazikulu,+Ndipo sachita zinthu zosemphana ndi chilungamo+ chake komanso kulungama kwake kodabwitsa.+
23 Wamphamvuyonse sitingathe kumumvetsa.+Iye ali ndi mphamvu zazikulu,+Ndipo sachita zinthu zosemphana ndi chilungamo+ chake komanso kulungama kwake kodabwitsa.+