Yobu 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tsopano ndadziwa kuti inu mumatha kuchita zinthu zonse,Ndiponso kuti palibe chilichonse chimene mukufuna kuchita chimene simungakwanitse.+ Yobu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:2 Nsanja ya Olonda,4/15/2001, tsa. 11
2 “Tsopano ndadziwa kuti inu mumatha kuchita zinthu zonse,Ndiponso kuti palibe chilichonse chimene mukufuna kuchita chimene simungakwanitse.+