Yobu 42:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nʼchifukwa chake ndikubweza mawu anga,+Ndipo ndikulapa mufumbi ndi mʼphulusa.”+