-
Yobu 42:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Tsopano utenge ngʼombe zamphongo 7 ndi nkhosa zamphongo 7. Upite nazo kwa mtumiki wanga Yobu, ndipo inuyo mukapereke nsembe yopsereza chifukwa cha tchimo lanu. Ndiyeno Yobu mtumiki wanga akakupemphererani.+ Ndithudi ineyo ndidzayankha pempho lake* kuti ndisakuchitireni zinthu mogwirizana ndi zopusa zimene mwachita, chifukwa simunanene zoona zokhudza ine ngati mmene wachitira mtumiki wanga Yobu.”
-