Salimo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma si mmene oipa alili.Iwo ali ngati mankhusu* amene amauluzika ndi mphepo. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:4 Nsanja ya Olonda,7/15/2004, ptsa. 13-14